otherhindi

daily worship

Share:

daily worship

Tap to play

Lyrics with Meaning

View lyrics page →

Original

I have never seen, no one like you (no one like you) No one like you (no one like you) Yesu (Yesu)

Verse 2

Original

I have never seen, no one like you (no one like you) No one like you (no one like you) Yesu (Yesu)

Ambuye (Ambuye)

Original

Ambuye (Ambuye) Ndikuthokoza Ambuye (Ndikuthokoza Ambuye) Ambuye (Ambuye)

Verse 4

Original

Ambuye (Ambuye), Ndikuthokoza Ambuye Eeh eh eh

Verse 5

Original

Iyi ndi nyimbo yafuko langa, my daily worship Ndikuvutika simunandisiye chonchi Kundionesa ufumu wanu kundipasa chi plot Nde kulikose ndingapiteko tili limodzi

Abale ndi alongo zikavuta amathawa

Original

Mavuto, pa mtendele simumansintha ma colour Nde zingavute bwanji ndimayesesa ndisadande Poti masiku sakoma onse, ndi nthawi chabe

Verse 7

Original

Iyi ndi daily worship, nyimbo yafuko langa Kenako ukamvera uzipezamo ka bata Osamathamangila kunena kuti sanayankhe

Verse 8

Original

Chifukwa olo mpweya tikupumau ndi wake Pali chinthu chimodzi chomwe mumalakwisa brazi

Verse 9

Original

Mufuna mudwale kaye kuti muyamikire nthanzi Wina amwalire kuti muyamikire moyo Akachedwa kuyankha mumasiya kukhala loyal

Verse 10

Original

Ndeno Tate wanga ndufuna kukhala munthu wa humble Poti ndikuziwa mumapasa, mumalanda

Verse 11

Original

Komanso ndukufuna ndikhale chitsanzo Mfana wa mature poti chibwana chimalanda

Verse 12

Original

Kuchepesa anga, bible likhale mzanga Munthu kundiyamba ine kukhululuka nsanga

Verse 13

Original

Kupewa ma blanda, Jajah mu mtima mwanga Tsiku lomalidza kuchongetsa dzina langa

Ambuye (yea yea yea yea)

Original

Ambuye (yea yea yea yea) Ndikuthokoza Ambuye (Ndikuthokoza Ambuye)

Ambuye (yea yea yea yea)

Original

Ambuye (yea yea yea yea) Ndikuthokoza Ambuye (Ambuye eeh) Uuh uh uuh

Verse 16

Original

I have never seen, no one like you (no one like you) No one like you (no one like you) Yesu (Yesu)

Verse 17

Original

I have never seen, no one like you (no one like you) No one like you (no one like you) Yesu (Yesu)

Ambuye

Original

Ambuye (no one like you) Ndikuthokoza Ambuye (Yesu)

Ambuye

Original

Ambuye (no one like you) Ndikuthokoza Ambuye (Yesu) Uuh yeah yeah Uuh yeah yeah

Gwamba

Get the daily panchang & festival updates

Join our free newsletter, no spam, unsubscribe anytime.